2 Mafumu 17:10 BL92

10 Nadziimikira zoimiritsa ndi zifanizo pa citunda ciri conse cacitali, ndi patsinde pa mtengo uli wonse wogudira;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:10 nkhani