2 Mafumu 17:17 BL92

17 Napititsa ana ao amuna ndi akazi kumoto, naombeza ula, nacita zanyanga, nadzigulitsa kucita coipa pamaso pa Yehova, kuutsa mkwiyo wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:17 nkhani