2 Mafumu 17:18 BL92

18 Cifukwa cace Yehova anakwiya naye Israyeli kwakukuru, nawacotsa pamaso pace osatsala mmodzi, koma pfuko la Yudalokha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:18 nkhani