2 Mafumu 17:20 BL92

20 Ndipo Yehova anakaniza mbumba yonse ya Israyeli, nawazunza, nawapereka m'dzanja la ofunkha, mpaka anawataya pamaso pace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:20 nkhani