2 Mafumu 17:23 BL92

23 mpaka Yehova adacotsa Israyeli pamaso pace, monga adanena mwa dzanja la atumiki ace onse aneneriwo. Momwemo Israyeli anacotsedwa m'dziko lao kumka nao ku Asuri mpaka lero lino.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:23 nkhani