27 Pamenepo mfumu ya Asuri analamulira, kuti, Mukani naye komweko wina wa ansembe munawacotsako, nakakhale komweko, akawalangize makhalidwe a Mulungu wa dzikoli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17
Onani 2 Mafumu 17:27 nkhani