28 Nadza wina wa ansembewo adawacotsa ku Samariya, nakhala ku Beteli, nawalangiza m'mene azimuopera Yehova.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17
Onani 2 Mafumu 17:28 nkhani