2 Mafumu 17:29 BL92

29 Koma a mtundu uli wonse anapanga milungu yao yao, naiika m'nyumba za misanje adazimanga Asamariya, a mtundu uli wonse m'midzi mwao mokhala iwo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:29 nkhani