2 Mafumu 17:30 BL92

30 Ndipo anthu a Babulo anapanga Sukoti Bemoti, ndi anthu a Kuta anapanga Nerigali, ndi anthu a Hamati anapanga Asima,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:30 nkhani