2 Mafumu 18:11 BL92

11 Ndipo mfumu ya Asuri anacotsa Aisrayeli kumka nao ku Asuri, nawakhalitsa m'Hala, ndi m'Habori, ku mtsinje wa Gozani, ndi m'midzi ya Amedi;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:11 nkhani