12 cifukwa sanamvera mau a Yehova Mulungu wao, koma analakwira cipangano cace, ndico zonse anazilamulira Mose mtumiki wa Yehova; sanazimvera kapena kuzicita.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18
Onani 2 Mafumu 18:12 nkhani