2 Mafumu 18:16 BL92

16 Nthawi yomweyi Hezekiya anakanganula golidi wa pa zitseko za Kacisi wa Yehova, ndi pa zimphuthu adazikuta Hezekiya mfumu ya Yuda, nampereka kwa mfumu ya Asuri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:16 nkhani