30 kapena Hezekiya asakukhulupiritseni pa Yehova, ndi kuti, Yehova adzatilanditsa ndithu, ndi mudzi uwu sudzaperekedwa m'dzanja la mfumu ya Asuri.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18
Onani 2 Mafumu 18:30 nkhani