31 Musamvere Hezekiya; pakuti Itero mfumu ya Asuri, Mupangane nane zamtendere, nimuturukire kwa ine, ndi kumadya yense ku mpesa wace, ndi yense ku mkuyu wace, ndi kumwa yense madzi a m'citsime cace;
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18
Onani 2 Mafumu 18:31 nkhani