34 Iri kuti milungu ya Hamati, ndi ya Aripadi? iri kuti milungu ya Sefaravaimu, kapena Hena, ndi Iva? Kodi yalanditsa Samariya m'dzanja langa?
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18
Onani 2 Mafumu 18:34 nkhani