6 Pakuti anaumirira Yehova osapambuka pambuyo pace, koma anasunga malamulo amene Yehova adawalamulira Mose.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18
Onani 2 Mafumu 18:6 nkhani