2 Mafumu 19:11 BL92

11 Taona, udamva ico mafumu a Asuri anacitira maiko onse, ndi kuwaononga konse; ndipo uti upulumuke ndiwe kodi?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19

Onani 2 Mafumu 19:11 nkhani