12 Kodi milunguyaamitundu inawalanditsa amene makolo anga anawaononga, ndiwo Gozani, ndi Hara Rezefi, ndi ana a Edeni okhala m'Telasara?
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:12 nkhani