19 Ndipo tsono, Yehova Mulungu wathu, mutipulumutse m'dzanja lace, kuti adziwe maufumu onse a dziko lapansi kuti Inu ndinu Yehova Mulungu, Inu nokha nokha.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:19 nkhani