21 Mau a Yehova akumnenera iye ndi awa, Namwali mwana wamkazi wa Ziyoni akunyoza, akuseka mwana wamkazi wa Yerusalemu, akupukusira mutu pambuyo pako.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:21 nkhani