22 Ndiye yani wamtonza ndi kumcitira mwano? ndiye yani wamkwezera mau ndi kumgadamira maso ako m'mwamba? Ndiye Woyerayo wa Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:22 nkhani