31 Pakuti ku Yerusalemu kudzaturuka otsala, ndi akupulumukawo ku phiri la Ziyoni; cangu ca Yehova cidzacita ici.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:31 nkhani