32 Cifukwa cace atero Yehova za mfumu ya Asuri, iye sadzalowa m'mudzi muno, kapena kuponyamo mubvi, kapena kufikako ndi cikopa, kapena kuundira mtumbira.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19
Onani 2 Mafumu 19:32 nkhani