2 Mafumu 19:37 BL92

37 Ndipokunali popembedza iye m'nyumba ya Nisiroki mulungu wace, Adrameleki ndi Sarezere anamkantha ndi lupanga; napulumukira ku dziko la Ararati. Ndipo Esarihadoni mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19

Onani 2 Mafumu 19:37 nkhani