2 Mafumu 2:11 BL92

11 Ndipo kunacidka, akali ciyendere ndi kukambirana, taonani, anaoneka gareta wamoto ndi akavalo amoto, nawalekanitsa awiriwa; Eliya nakwera kumwamba ndi kabvumvulu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:11 nkhani