2 Mafumu 2:12 BL92

12 Ndipo Elisa anapenya, napfuula, Atate wanga, atate wanga, gareta wa Israyeli ndi apakavalo ace! Koma analibe kumpenyanso; nagwira zobvala zace zace, nazing'amba pakati.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:12 nkhani