2 Mafumu 2:14 BL92

14 Ndipo anatenga copfunda ca Eliya cidamtayikiraco, napanda madziwo, nati, Ali kuti Yehova Mulungu wa Eliya? Ndipo atapanda madziwo anagawikana kwina ndi kwina, naoloka Elisa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:14 nkhani