2 Mafumu 2:15 BL92

15 Ndipo pamene anampenya ana a aneneri okhala ku Yeriko pandunji pace, anati, Mzimu wa Eliya watera pa Elisa. Ndipo anadza kukomana naye, nadziweramitsa pansi kumaso kwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:15 nkhani