2 Mafumu 2:16 BL92

16 Ndipo ananena naye, Taonani, tsono anyamata anufe tiri nao amuna makumi asanu amphamvu, amuke kukafuna mbuye wanu; kapena wamkweza mzimu wa Yehova ndi kumponya pa phiri lina, kapena m'cigwa dna. Koma anati, Musatumiza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:16 nkhani