17 Koma anamuumiriza kufikira anacita manyazi; pamenepo anati, Tumizani. Motero anatumiza amuna makumi asanu, namfunafuna iwo masiku atatu, osampeza.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2
Onani 2 Mafumu 2:17 nkhani