2 Mafumu 2:18 BL92

18 Nabwerera kwa iye ali cikhalire ku Yeriko, ndipo anati kwa iwo, Kodi sindinanena nanu, Musamuka?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:18 nkhani