6 Ndipo Eliya ananena naye, Ukhale pompano, pakuti Yehova wandituma ku Yordano, Nati iye, Pali Mulungu, pali inu, sindikusiyani. Napitirira iwo awiri.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2
Onani 2 Mafumu 2:6 nkhani