2 Mafumu 2:5 BL92

5 Pamenepo ana a aneneri okhala ku Yeriko anayandikira kwa Elisa, nanena naye, Kodi udziwa kuti Yehova akucotsera lero mbuye wako, mtsogoleri wako? Nati iye, Inde ndidziwa, khalani muli cete.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:5 nkhani