4 Ndipo Eliya anati kwa iye, Elisa, ukhale pompano, pakuti Yehova wandituma ku Yeriko. Nati iye, Pali Yehova, pali inu, sindikusiyani. Motero anadza ku Yeriko.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2
Onani 2 Mafumu 2:4 nkhani