2 Mafumu 2:3 BL92

3 Ndipo ana a aneneri okhala ku Beteli anaturukira Elisa, nanena naye, Kodi udziwa kuti Yehova akucotsera lero mbuye wako, mtsogoleri wako? Nati, lode ndidziwa, khalani muli cete.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:3 nkhani