2 Mafumu 2:2 BL92

2 Ndipo Eliya anati kwa Elisa, Ukhale pompano pakuti Yehova wandituma ndimke ku Beteli. Nati Elisa, Pali Mulungu, pali inu, sindikusiyani. Motero anatsikira iwo ku Beteli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:2 nkhani