8 Ndipo Eliya anagwira copfunda cace, nacipindapinda napanda madzi, nagawikana kwina ndi kwina; ndipo anaoloka iwo onse awiri pansi pouma.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2
Onani 2 Mafumu 2:8 nkhani