2 Mafumu 2:9 BL92

9 Ndipo kunali ataoloka, Eliya anati kwa Elisa, Tapempha cimene ndikucitire ndisanacotsedwe kwa iwe. Ndipo Elisa anati, Mundipatse magawo awiri a mzimu wanu akhale pa ine.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:9 nkhani