2 Mafumu 20:11 BL92

11 Napfuulirakwa Yehova Yesayamneneriyo, nabweza iye mthunzi m'mbuyo makwerero khumi, ndiwo amene udatsikira pa makwerero a Ahazi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:11 nkhani