2 Mafumu 20:12 BL92

12 Nthawi ija Berodaki Baladani mwana wa Baladani mfumu ya Sabulo anatumiza akalata ndi mtulo kwa Hezekiya, popeza adamva kuti adadwala Hezekiya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:12 nkhani