2 Mafumu 20:3 BL92

3 Mukumbukile Yehova kuti ndinayendabe pamaso panu m'coonadi, ndi mtima wangwiro, ndi kucita zokoma m'kuona kwanu. Nalira Hezekiya kulira kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:3 nkhani