2 Mafumu 20:4 BL92

4 Ndipo kunali, asanaturukire Yesaya m'kati mwa mudzi, anamdzera mau a Yehova, ndi kuti,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:4 nkhani