2 Mafumu 21:1 BL92

1 Manase anali wa zaka khumi ndi ziwiri polowa iye ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi asanu ndi zisanu m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Hefisiba.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:1 nkhani