2 Mafumu 21:2 BL92

2 Ndipo anacita coipa pamaso pa Yehova, monga mwa zonyansa za amitundu amene Yehova anawaingitsa pamaso pa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:2 nkhani