2 Mafumu 21:3 BL92

3 Pakuti anamanganso misanje, imene Hezekiya atate wace adaiononga; nautsira Baala maguwa a nsembe, nasema cifanizo, monga anacita Ahabu mfumu ya Israyeli, nagwadira khamu lonse la kuthambo, nalitumikira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:3 nkhani