2 Mafumu 21:19 BL92

19 Amoni anali wa zaka makumi awiri mphambu ziwiri polowa iye ufumu wace, nakhala mfumu zaka ziwiri m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Mesulemeti mwana wa Haruzi wa ku Yotiba.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:19 nkhani