8 Ndipo sindidzacotsanso mapazi a Israyeli m'dziko ndidalipereka kwa makolo ao; cokhaci asamalire kucita monga mwa zonse ndawalamulira ndi monga mwa cilamulo conse anawalamulira Mose mtumiki wanga.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21
Onani 2 Mafumu 21:8 nkhani