2 Mafumu 21:7 BL92

7 Ndipo anaika cifanizo cosema cimene adacipanga m'nyumba ija Yehova adainenera kwa Davide ndi kwa Solomo mwana wace kuti, M'nyumba muno ndi m'Yerusalemu umene ndausankha mwa mafuko onse a Israyeli ndidzaikamo dzina langa kosatha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:7 nkhani