2 Mafumu 21:6 BL92

6 Napititsa mwana wace pamoto, naombeza maula, nacita zanyanga, naika obwebweta ndi openda; anacita zoipa zambiri pamaso pa Yehova kuutsa mkwiyo wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:6 nkhani