8 Ndipo Hilikiya mkulu wa ansembe anati kwa Safani mlembi, Ndapeza buku la cilamulo m'nyumba ya Yehova. Napereka Hilikiya bukulo kwa Safani, iye naliwerenga.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 22
Onani 2 Mafumu 22:8 nkhani